Ndipo munthu wina wa komweko anayankha nati, Ndipo atate wao ndiye yani? Chifukwa chake mauwa anakhala ngati mwambi, Kodi Saulonso ali mwa aneneri?
1 Samueli 10:13 - Buku Lopatulika Ndipo pamene adatha kunenera anafika kumsanjeko. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo pamene adatha kunenera anafika kumsanjeko. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Atatha kulosako, Saulo adapita ku kachisi ku phiri. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Sauli atasiya kuloserako, anapita ku kachisi ku phiri. |
Ndipo munthu wina wa komweko anayankha nati, Ndipo atate wao ndiye yani? Chifukwa chake mauwa anakhala ngati mwambi, Kodi Saulonso ali mwa aneneri?
Ndipo mbale wa atate wake wa Saulo ananena kwa iye ndi mnyamata wake, Munanka kuti? Ndipo iye anati, Kukafuna abuluwo; ndipo pakuona kuti sitinawapeze, tinadza kwa Samuele.