Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 9:4 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

4 Choncho Mose anawuza Aisraeli kuti azichita Paska,

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

4 Ndipo Mose ananena ndi ana a Israele, kuti achite Paska.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

4 Ndipo Mose ananena ndi ana a Israele, kuti achite Paska.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

4 Choncho Mose adauza Aisraele kuti azichita Paska.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 9:4
3 Mawu Ofanana  

Ndipo Mose anasonkhanitsa akuluakulu onse a Israeli nati, “Pitani msanga kukasankha nkhosa zokwanira pa mabanja anu, ndipo muziphe ngati Paska.


Muzichita Paska pa nthawi yake yoyikika, madzulo a tsiku la 14 la mwezi uno, potsata malamulo ndi malangizo ake.”


ndipo anachitadi Paskayo mʼchipululu cha Sinai madzulo a tsiku la 14 la mwezi woyamba. Aisraeli anachita zonse monga momwe Yehova analamulira Mose.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa