Numeri 9:1 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Yehova anayankhula ndi Mose mʼchipululu cha Sinai pa mwezi woyamba wa chaka chachiwiri atatuluka mu Igupto, nati, Onani mutuwoBuku Lopatulika1 Ndipo Yehova ananena ndi Mose m'chipululu cha Sinai, mwezi woyamba wa chaka chachiwiri atatuluka m'dziko la Ejipito, ndi kuti, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo Yehova ananena ndi Mose m'chipululu cha Sinai, mwezi woyamba wa chaka chachiwiri atatuluka m'dziko la Ejipito, ndi kuti, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Pa mwezi woyamba wa chaka chachiŵiri Aisraele atatuluka m'dziko la Ejipito, Chauta adauza Mose m'chipululu cha Sinai kuti, Onani mutuwo |