Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 7:83 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

83 ngʼombe zazimuna ziwiri, nkhosa zazimuna zisanu, mbuzi zazimuna zisanu, ndi ana ankhosa aamuna asanu a chaka chimodzi, nsembe yachiyanjano. Ichi chinali chopereka cha Ahira mwana wa Enani.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

83 ndi nsembe yoyamika, ng'ombe ziwiri, nkhosa zamphongo zisanu, atonde asanu, anaankhosa asanu a chaka chimodzi; ichi ndi chopereka cha Ahira mwana wa Enani.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

83 ndi nsembe yoyamika, ng'ombe ziwiri, nkhosa zamphongo zisanu, atonde asanu, anaankhosa asanu a chaka chimodzi; ichi ndi chopereka cha Ahira mwana wa Enani.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

83 Ndipo zoperekera nsembe yachiyanjano zinali ng'ombe ziŵiri, nkhosa zamphongo zisanu, atonde asanu, ndi anaankhosa asanu amphongo a chaka chimodzi. Zimenezi ndizo zinali zopereka za Ahira mwana wa Enani.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 7:83
4 Mawu Ofanana  

Ahira mwana wa Enani, kuchokera ku fuko la Nafutali.”


Lotsatira lidzakhala fuko la Nafutali. Mtsogoleri wa Anafutali ndi Ahira mwana wa Enani.


mbuzi yayimuna imodzi ya nsembe yopepesera machimo;


Zopereka za atsogoleri a Israeli zopatulira guwa lansembe pamene linadzozedwa zinali izi: mbale khumi ndi ziwiri zasiliva, mabeseni owazira asiliva khumi ndi awiri ndi mbale zagolide khumi ndi ziwiri.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa