Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 7:81 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

81 mwana wangʼombe wamwamuna mmodzi, nkhosa imodzi yayimuna ndi mwana wankhosa mmodzi wa chaka chimodzi, nsembe yopsereza;

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

81 ng'ombe yamphongo imodzi, nkhosa yamphongo imodzi, mwanawankhosa mmodzi wa chaka chimodzi, zikhale nsembe yopsereza;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

81 ng'ombe yamphongo imodzi, nkhosa yamphongo imodzi, mwanawankhosa mmodzi wa chaka chimodzi, zikhale nsembe yopsereza;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

81 mwanawang'ombe mmodzi wamphongo, nkhosa yamphongo imodzi, ndiponso mwanawankhosa wamphongo wa chaka chimodzi, kuti zonsezo aperekere nsembe yopsereza;

Onani mutuwo Koperani




Numeri 7:81
2 Mawu Ofanana  

mbale imodzi yagolide yolemera magalamu 110, yodzaza ndi lubani;


mbuzi yayimuna imodzi ya nsembe yopepesera machimo;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa