Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 7:71 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

71 ndi ngʼombe ziwiri zazimuna, nkhosa zazimuna zisanu, mbuzi zazimuna zisanu, ndi ana ankhosa aamuna asanu a chaka chimodzi, nsembe yachiyanjano. Ichi chinali chopereka cha Ahiyezeri mwana wa Amisadai.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

71 ndi nsembe yoyamika, ng'ombe ziwiri, nkhosa zamphongo zisanu, atonde asanu, anaankhosa asanu a chaka chimodzi; ndicho chopereka cha Ahiyezere mwana wa Amisadai.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

71 ndi nsembe yoyamika, ng'ombe ziwiri, nkhosa zamphongo zisanu, atonde asanu, anaankhosa asanu a chaka chimodzi; ndicho chopereka cha Ahiyezere mwana wa Amisadai.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

71 Ndipo zoperekera nsembe yachiyanjano zinali ng'ombe ziŵiri, nkhosa zamphongo zisanu, atonde asanu, ndi anaankhosa asanu amphongo a chaka chimodzi. Zimenezi ndizo zinali zopereka za Ahiyezere mwana wa Amishadai.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 7:71
4 Mawu Ofanana  

Ahiyezeri mwana wa Amisadai, kuchokera ku fuko la Dani,


Kumpoto kudzakhala msasa wa magulu a Dani pamene pali mbendera yawo. Mtsogoleri wa Adani ndi Ahiyezeri mwana wa Amisadai.


mbuzi yayimuna imodzi ya nsembe yopepesera machimo;


Pa tsiku la khumi ndi chimodzi, Pagieli mwana wa Okirani, mtsogoleri wa fuko la Aseri, anabweretsa chopereka chake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa