Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 7:70 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

70 mbuzi yayimuna imodzi ya nsembe yopepesera machimo;

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

70 tonde mmodzi akhale nsembe yauchimo;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

70 tonde mmodzi akhale nsembe yauchimo;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

70 Adaperekanso tonde mmodzi woperekera nsembe yopepesera machimo.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 7:70
2 Mawu Ofanana  

mwana wangʼombe wamwamuna mmodzi, nkhosa imodzi yayimuna ndi mwana wankhosa mmodzi wa chaka chimodzi, nsembe yopsereza;


ndi ngʼombe ziwiri zazimuna, nkhosa zazimuna zisanu, mbuzi zazimuna zisanu, ndi ana ankhosa aamuna asanu a chaka chimodzi, nsembe yachiyanjano. Ichi chinali chopereka cha Ahiyezeri mwana wa Amisadai.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa