Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 7:61 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

61 Chopereka chakecho chinali mbale imodzi yasiliva yolemera kilogalamu imodzi ndi theka ndi beseni limodzi lowazira lolemera magalamu 800, zonse monga mwa muyeso wa ku malo opatulika; zonse ziwiri zinali zodzaza ndi ufa wosalala wosakaniza ndi mafuta monga chopereka cha zakudya;

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

61 chopereka chake ndicho mbale imodzi yasiliva, kulemera kwake masekeli zana limodzi ndi makumi atatu, mbale yowazira imodzi ya masekeli makumi asanu ndi awiri, kuyesa sekeli wa malo opatulika; zonse ziwiri zodzala ndi ufa wosakaniza ndi mafuta, ukhale nsembe yaufa;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

61 chopereka chake ndicho mbale imodzi yasiliva, kulemera kwake masekeli zana limodzi ndi makumi atatu, mbale yowazira imodzi ya masekeli makumi asanu ndi awiri, kuyesa sekeli wa malo opatulika; zonse ziwiri zodzala ndi ufa wosanganiza ndi mafuta, ukhale nsembe yaufa;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

61 Iye adapereka mbale imodzi yasiliva yolemera kilogaramu limodzi ndi theka, mkhate wasiliva wa magaramu 800, potsata muyeso wa ku malo opatulika. Ziŵiri zonsezo zinali zodzaza ndi ufa wosalala wosakaniza ndi mafuta, za chopereka cha chakudya.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 7:61
3 Mawu Ofanana  

Pa tsiku lachisanu ndi chinayi Abidani mwana wa Gideoni mtsogoleri wa fuko la Benjamini, anabweretsa chopereka chake.


mbale imodzi yagolide yolemera magalamu 110, yodzaza ndi lubani;


Ndipo atamupangira amayi ake anati, “Mundipatse pomwe pano mutu wa Yohane Mʼbatizi mʼmbale.”


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa