Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 7:54 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

54 Pa tsiku lachisanu ndi chitatu Gamalieli mwana wa Pedazuri, mtsogoleri wa fuko Manase, anabweretsa chopereka chake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

54 Tsiku lachisanu ndi chitatu kalonga wa ana a Manase ndiye Gamaliele mwana wa Pedazuri:

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

54 Tsiku lachisanu ndi chitatu kalonga wa ana a Manase ndiye Gamaliele mwana wa Pedazuri:

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

54 Tsiku lachisanu ndi chitatu linali la Gamaliele mwana wa Pedazuri, mtsogoleri wa Amanase.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 7:54
4 Mawu Ofanana  

Mwa ana a Yosefe: kuchokera ku fuko la Efereimu, Elisama mwana wa Amihudi; kuchokera ku fuko la Manase, Gamalieli mwana wa Pedazuri;


Fuko la Manase lidzakhala pafupi ndi Efereimu. Mtsogoleri wa Amanase ndi Gamalieli mwana wa Pedazuri.


ngʼombe ziwiri, nkhosa zazimuna zisanu, mbuzi zazimuna zisanu ndi ana ankhosa aamuna asanu a chaka chimodzi, nsembe yachiyanjano. Ichi chinali chopereka cha Elisama mwana wa Amihudi.


Chopereka chakecho chinali mbale imodzi yasiliva yolemera kilogalamu imodzi ndi theka, ndi beseni limodzi lowazira lasiliva lolemera magalamu 800, zonse monga mwa muyeso wa ku malo opatulika; zonse ziwiri zinali zodzaza ndi ufa wosalala wosakaniza ndi mafuta monga chopereka chachakudya;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa