Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 7:53 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

53 ngʼombe ziwiri, nkhosa zazimuna zisanu, mbuzi zazimuna zisanu ndi ana ankhosa aamuna asanu a chaka chimodzi, nsembe yachiyanjano. Ichi chinali chopereka cha Elisama mwana wa Amihudi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

53 ndi nsembe yoyamika, ng'ombe ziwiri, nkhosa za mphongo zisanu, atonde asanu, anaankhosa asanu a chaka chimodzi; ndicho chopereka cha Elisama mwana wa Amihudi.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

53 ndi nsembe yoyamika, ng'ombe ziwiri, nkhosa za mphongo zisanu, atonde asanu, anaankhosa asanu a chaka chimodzi; ndicho chopereka cha Elisama mwana wa Amihudi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

53 Ndipo zoperekera nsembe yachiyanjano zinali ng'ombe ziŵiri, nkhosa zamphongo zisanu, atonde asanu, ndi anaankhosa asanu amphongo a chaka chimodzi. Zimenezi ndizo zimene zinali zopereka za Alisama mwana wa Amihudi.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 7:53
4 Mawu Ofanana  

Mwa ana a Yosefe: kuchokera ku fuko la Efereimu, Elisama mwana wa Amihudi; kuchokera ku fuko la Manase, Gamalieli mwana wa Pedazuri;


Kumadzulo kudzakhala magulu a msasa wa Efereimu pamene pali mbendera yawo. Mtsogoleri wa Aefereimuwo ndi Elisama mwana wa Amihudi.


mbuzi imodzi ya nsembe yopepesera machimo;


Pa tsiku lachisanu ndi chitatu Gamalieli mwana wa Pedazuri, mtsogoleri wa fuko Manase, anabweretsa chopereka chake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa