Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 7:51 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

51 mwana wangʼombe wamwamuna mmodzi, nkhosa imodzi yayimuna ndi mwana wankhosa wamwamuna mmodzi wa chaka chimodzi, nsembe yopsereza;

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

51 ng'ombe yamphongo imodzi, nkhosa yamphongo imodzi, mwanawankhosa mmodzi wa chaka chimodzi, zikhale nsembe yopsereza;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

51 ng'ombe yamphongo imodzi, nkhosa yamphongo imodzi, mwanawankhosa mmodzi wa chaka chimodzi, zikhale nsembe yopsereza;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

51 mwanawang'ombe mmodzi wamphongo, nkhosa yamphongo imodzi, ndiponso mwanawankhosa mmodzi wamphongo wa chaka chimodzi, kuti zonsezo aperekere nsembe yopsereza.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 7:51
2 Mawu Ofanana  

Kodi ndidzatenga chiyani kupita nacho pamaso pa Yehova ndi kukagwada pamaso pa Mulungu wakumwamba? Kodi ndidzabwera pamaso pake ndi nsembe yopsereza, ndi ana angʼombe a chaka chimodzi?


mbuzi imodzi ya nsembe yopepesera machimo;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa