Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 7:41 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

41 ngʼombe ziwiri, nkhosa zisanu, mbuzi zazimuna zisanu ndi ana ankhosa aamuna asanu a chaka chimodzi, nsembe yachiyanjano. Ichi chinali chopereka cha Selumieli mwana wa Zurisadai.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

41 ndi nsembe yoyamika, ng'ombe ziwiri, nkhosa zamphongo zisanu, atonde asanu, anaankhosa asanu a chaka chimodzi; ndicho chopereka cha Selumiele mwana wa Zurishadai.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

41 ndi nsembe yoyamika, ng'ombe ziwiri, nkhosa zamphongo zisanu, atonde asanu, anaankhosa asanu a chaka chimodzi; ndicho chopereka cha Selumiele mwana wa Zurishadai.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

41 Ndipo zoperekera nsembe yachiyanjano zinali ng'ombe ziŵiri, nkhosa zamphongo zisanu, atonde asanu ndi anaankhosa asanu amphongo a chaka chimodzi. Zimenezi ndizo zinali zopereka za Selumiele mwana a Zurishadai.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 7:41
4 Mawu Ofanana  

Selumieli mwana wa Zurisadai, kuchokera ku fuko la Simeoni,


Fuko la Simeoni lidzamanga pafupi ndi Rubeni. Mtsogoleri wa gulu la Simeoni ndi Selumieli mwana wa Zurisadai.


mbuzi imodzi ya nsembe yopepesera machimo;


Pa tsiku lachisanu ndi chimodzi, Eliyasafu mwana wa Deuweli, mtsogoleri wa fuko la Gadi, anabweretsa chopereka chake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa