Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 7:23 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

23 ndi ngʼombe ziwiri, nkhosa zazimuna ziwiri, mbuzi zazimuna zisanu ndi ana ankhosa asanu a chaka chimodzi, nsembe ya chiyanjano. Ichi chinali chopereka cha Netanieli mwana wa Zuwara.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

23 ndi nsembe yoyamika, ng'ombe ziwiri, nkhosa zamphongo zisanu, atonde asanu, anaankhosa asanu a chaka chimodzi; ndicho chopereka cha Netanele mwana wa Zuwara.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

23 ndi nsembe yoyamika, ng'ombe ziwiri, nkhosa zamphongo zisanu, atonde asanu, anaankhosa asanu a chaka chimodzi; ndicho chopereka cha Netanele mwana wa Zuwara.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

23 Ndipo zoperekera nsembe yachiyanjano zinali ng'ombe ziŵiri, nkhosa zisanu zamphongo, atonde asanu, ndi anaankhosa asanu amphongo a chaka chimodzi. Zimenezi ndizo zinali zopereka za Netanele mwana wa Zuwara.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 7:23
8 Mawu Ofanana  

Solomoni anapereka nsembe zachiyanjano kwa Yehova: ngʼombe 22,000, nkhosa ndi mbuzi 120,000. Motero mfumu pamodzi ndi Aisraeli onse anapatula Nyumba ya Yehova.


“Ndinayenera kupereka nsembe zachiyanjano. Lero ndakwaniritsa malumbiro anga.


Netanieli mwana wa Zuwara, kuchokera ku fuko la Isakara,


Fuko la Isakara lidzamanga pafupi ndi Yuda. Mtsogoleri wa gulu la Isakara ndi Netanieli mwana wa Zuwara.


mbuzi yayimuna imodzi ya nsembe yotetezera machimo;


Pa tsiku lachitatu, Eliabu mwana wa Heloni, mtsogoleri wa Azebuloni, anabweretsa chopereka chake.


Paulo, mtumwi wa Khristu Yesu mwachifuniro cha Mulungu, ndi Timoteyo mʼbale wathu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa