Numeri 6:9 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 “Ngati munthu wina afa mwadzidzidzi pafupi naye ndi kudetsa tsitsi lake loperekedwalo, amete mutu wake pa tsiku lodziyeretsa, tsiku lachisanu ndi chiwiri. Onani mutuwoBuku Lopatulika9 Munthu akafa chikomo pali iye, ndipo akadetsa mutu wake wowinda; pamenepo azimeta mutu wake tsiku la kumyeretsa kwake, tsiku lachisanu ndi chiwiri aumete. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Munthu akafa chikomo pali iye, ndipo akadetsa mutu wake wowinda; pamenepo azimeta mutu wake tsiku la kumyeretsa kwake, tsiku lachisanu ndi chiwiri aumete. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 “Ngati munthu wina aliyense afa mwadzidzidzi pafupi naye, ndipo pakutero aipitsa tsitsi lake loperekedwalo, amete kumutu kwake pa tsiku lachisanu ndi chiŵiri, tsiku lomuyeretsa. Onani mutuwo |