Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 6:7 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

7 Ngakhale abambo ake kapena amayi ake kapena mchimwene wake kaya mchemwali wake atamwalira, asadzidetse pokhudza mitembo yawo chifukwa kulumbira kwake kwa kudzipatula yekha kwa Yehova kuli pamutu pake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

7 Asadzidetse ndi atate wake, kapena mai wake, mbale wake, kapena mlongo wake, akafa iwowa; popeza chowindira Mulungu wake chili pamutu pake.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

7 Asadzidetse ndi atate wake, kapena mai wake, mbale wake, kapena mlongo wake, akafa iwowa; popeza chowindira Mulungu wake chili pamutu pake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

7 Asadziipitse poyandikira mtembo wa bambo wake, wa mai wake, wa mbale wake kapena wa mlongo wake, chifukwa kulumbira kwa kudzipereka kwake kwa Mulungu kuli pamutu pake.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 6:7
5 Mawu Ofanana  

“ ‘Wansembe asadziyipitse pokhudza munthu wakufa, pokhapokha ngati wakufayo ndi abambo ake kapena amayi ake, mwana wake wamwamuna kapena wamkazi, mʼbale wake kapena mlongo wake wosakwatiwa.


Munthuyo ndi wopatulika masiku onse odzipereka kwake kwa Yehova.


Koma ena a iwo sanathe kuchita nawo Paska pa tsiku limenelo chifukwa anali odetsedwa chifukwa chokhudza mtembo. Choncho anabwera kwa Mose ndi Aaroni tsiku lomwelo,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa