Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 5:4 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

4 Aisraeli anachitadi zimenezi. Anawatulutsira kunja kwa msasa monga momwe Yehova analamulira Mose.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

4 Ndipo ana a Israele anachita chotero, nawatulutsira kunja kwa chigono; monga Yehova adanena ndi Mose momwemo ana a Israele anachita.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

4 Ndipo ana a Israele anachita chotero, nawatulutsira kunja kwa chigono; monga Yehova adanena ndi Mose momwemo ana a Israele anachita.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

4 Tsono Aisraele adachitadi zimenezi, ndipo adaŵatulutsira kunja anthuwo. Ankachitadi monga momwe Chauta adaauzira Mose.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 5:4
5 Mawu Ofanana  

Mfumu Uziya anali ndi khate mpaka tsiku limene anamwalira. Iye amakhala mʼnyumba ya yekha ngati wakhate, ndipo samalowa mʼNyumba ya Yehova. Yotamu mwana wake ndiye amayangʼanira nyumba yaufumu ndipo ankalamulira anthu a mʼdzikomo.


Aisraeli anachita monga momwe Yehova analamulira Mose ndi Aaroni.


“Aisraeli onse anachita monga momwe Yehova analamulira Mose ndi Aaroni.


Muchotse amuna komanso amayi ndipo muwatulutsire kunja kwa msasa kuti asadetse msasa wawo kumene Ine ndimakhala pakati pawo.”


Yehova anati kwa Mose,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa