Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 5:11 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

11 Kenaka Yehova anawuza Mose kuti,

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

11 Ndipo Yehova ananena ndi Mose, nati,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

11 Ndipo Yehova ananena ndi Mose, nati,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

11 Chauta adauza Mose kuti,

Onani mutuwo Koperani




Numeri 5:11
3 Mawu Ofanana  

Umu ndi mʼmene mkazi amachitira atachita chigololo: Atatha kudya ndi kupukuta pakamwa pake iye amanena kuti “Sindinachite kalikonse kolakwa.”


Mphatso zilizonse zopatulika ndi za munthuyo, koma zomwe wapereka kwa wansembe ndi za wansembeyo.’ ”


“Yankhula ndi Aisraeli ndipo uwawuze kuti, ‘Ngati mkazi wa munthu wina ayenda njira yosayenera nakhala wosakhulupirika kwa mwamuna wake,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa