Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 4:8 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 Tsono pamwamba pa izi aziyalapo nsalu yofiira, ndi kuzikuta mʼzikopa za akatumbu ndi kuyika mitengo yonyamulira mʼmalo mwake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

8 Ndipo ayale pa izi nsalu yofiira, ndi kuliphimba ndi chophimba cha zikopa za akatumbu, ndi kupisako mphiko zake.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 Ndipo ayale pa izi nsalu yofiira, ndi kuliphimba ndi chophimba cha zikopa za akatumbu, ndi kupisako mphiko zake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 Tsono pamwamba pa zimenezo ayalepo nsalu yofiira, ndi kuziphimba zonsezo ndi zikopa zambuzi, ndipo apise mphiko m'zigwinjiri zake.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 4:8
5 Mawu Ofanana  

“Upange tebulo la matabwa amtengo wa mkesha, mulitali mwake masentimita 91, mulifupi mwake masentimita 46, msinkhu wake masentimita 69.


zikopa za nkhosa zazimuna za utoto wofiira ndi zikopa za akatumbu; matabwa amtengo wa mkesha;


“Azitenga nsalu ya mtundu wa thambo ndi kukutira choyikapo nyale, pamodzi ndi nyale zake, zopanira zake, zotengera zake ndi mitsuko yonse yosungiramo mafuta.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa