Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 4:42 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

42 Amerari anawawerenga monga mwa mafuko ndi mabanja awo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

42 Ndipo owerengedwa a mabanja a ana a Merari, monga mwa mabanja ao, monga mwa nyumba za makolo ao,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

42 Ndipo owerengedwa a mabanja a ana a Merari, monga mwa mabanja ao, monga mwa nyumba za makolo ao,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

42 Adaŵerenganso ana a Merari potsata mabanja ao ndiponso banja la makolo ao,

Onani mutuwo Koperani




Numeri 4:42
4 Mawu Ofanana  

mwana wa Mahili, mwana wa Musi, mwana wa Merari, mwana wa Levi.


Ndipo anazigawa kwa ansembe amene analembetsa mayina awo mwa mbiri ya mabanja awo, chimodzimodzinso Alevi amene anali ndi zaka makumi awiri kapena kupitirira molingana ndi udindo wawo ndi magulu awo.


Ichi chinali chiwerengero cha Ageresoni mwa mabanja awo amene ankatumikira ku tenti ya msonkhano. Mose ndi Aaroni anawawerenga monga mwa lamulo la Yehova.


Amuna onse kuyambira zaka makumi atatu mpaka makumi asanu amene anabwera kudzatumikira ntchito mu tenti ya msonkhano,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa