Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 32:2 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 Choncho Arubeni ndi Agadi anapita kwa Mose ndi kwa wansembe Eliezara ndi kwa atsogoleri a anthu ndi kunena kuti,

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

2 Pamenepo ana a Gadi ndi ana a Rubeni anadza nanena ndi Mose, ndi Eleazara wansembe, ndi akalonga a khamulo, nati,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 Pamenepo ana a Gadi ndi ana a Rubeni anadza nanena ndi Mose, ndi Eleazara wansembe, ndi akalonga a khamulo, nati,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 Choncho ana a Gadi ndi ana a Rubeni aja adabwera kwa Mose, kwa wansembe Eleazara ndi kwa atsogoleri a mpingo, naŵauza kuti,

Onani mutuwo Koperani




Numeri 32:2
6 Mawu Ofanana  

“ ‘Ngati mtsogoleri achimwa mosadziwa nachita zimene ndi zoletsedwa ndi Yehova Mulungu wake, ndiye kuti wapalamula.


Arubeni ndi Agadi amene anali ndi ngʼombe zambiri ndi ziweto zina anaona dziko la Yazeri ndi la Giliyadi kuti linali labwino kwa ziwetozo.


“Ataroti, Diboni, Yazeri, Nimira, Hesiboni, Eleali, Sebamu, Nebo ndi Beoni,


Tsopano ugawire dziko limeneli mafuko asanu ndi anayi ndiponso theka la fuko la Manase, kuti likhale cholowa chawo.”


Choncho Aisraeli anapereka kwa fuko la Levi mizindayi pamodzi ndi malo odyetserako ziweto pogwiritsa ntchito maere, monga Yehova analamula kudzera mwa Mose.


Chifukwa chiyani munangokhala ku makola a nkhosa nʼkumangomvetsera zitoliro zoyitanira nkhosa? Pakati pa anthu a fuko la Rubeni panali kusinkhasinkha mtima kwambiri osadziwa chenicheni choyenera kuti achite.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa