Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 3:34 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

34 Chiwerengero cha amuna onse kuyambira a mwezi umodzi kapena kupitirirapo chinali 6,200.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

34 Ndipo owerengedwa ao, powerenga amuna onse, kuyambira a mwezi umodzi ndi mphambu, ndiwo zikwi zisanu ndi chimodzi kudza mazana awiri.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

34 Ndipo owerengedwa ao, powerenga amuna onse, kuyambira a mwezi umodzi ndi mphambu, ndiwo zikwi zisanu ndi chimodzi kudza mazana awiri.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

34 Chiŵerengero chao potsata kuchuluka kwa amuna onse, kuyambira mwana wamwamuna wa mwezi umodzi ndi wopitirirapo, chinali 6,200.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 3:34
5 Mawu Ofanana  

Chiwerengero cha anthu ochokera mʼfuko la Rubeni chinali 46,500.


Chiwerengero cha gulu lake lankhondo ndi 46,500.


Anthu onse aamuna mʼmisasa ya Yuda, chiwerengero chawo ndi 186,400 monga mwa magulu awo. Iwowo ndiwo aziyamba kusamuka.


Kwa Merari kunali banja la Mali ndi banja la Musi. Amenewa ndiye anali mabanja a Amerari.


Mtsogoleri wa magulu a mabanja a Amerari anali Zuriyeli mwana wa Abihaili. Iwo ankamanga misasa yawo kumpoto kwa Chihema.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa