Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 3:23 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

23 Mabanja a Ageresoni azimanga misasa yawo kumadzulo, kumbuyo kwa Chihema.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

23 Mabanja a Ageresoni azimanga mahema ao pambuyo pa chihema kumadzulo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

23 Mabanja a Ageresoni azimanga mahema ao pambuyo pa Kachisi kumadzulo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

23 Mabanja a Geresoni ankamanga zithando zao kumbuyo kwa chihema cha Mulungu mbali yakuzambwe.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 3:23
4 Mawu Ofanana  

Alevi nawonso, azimanga matenti awo mozungulira tenti yopatulika kuti chilango chisagwere Aisraeli onse. Ndipo Alevi aziyangʼanira ndi kusamalira tenti yopatulikayo.”


Tsono tenti ya msonkhano ndi msasa wa Alevi zidzakhala pakati pa misasayo. Iwo adzasamuka monga momwe anamangira misasa yawo, aliyense pa malo ake pamene pali mbendera yake.


Chiwerengero cha amuna onse amene anawawerenga a mwezi umodzi kapena kupitirirapo chinali 7,500.


Mtsogoleri wa mabanja a Ageresoni anali Eliyasafu mwana wa Laeli.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa