Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 3:14 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

14 Yehova anawuza Mose mʼchipululu cha Sinai kuti,

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

14 Ndipo Yehova ananena ndi Mose m'chipululu cha Sinai, nati

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

14 Ndipo Yehova ananena ndi Mose m'chipululu cha Sinai, nati

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

14 Chauta adauza Mose m'chipululu cha Sinai kuti,

Onani mutuwo Koperani




Numeri 3:14
3 Mawu Ofanana  

Ana a Levi anali awa: Geresoni, Kohati ndi Merari.


Ana a Israeli aja anafika ku chipululu cha Sinai pa tsiku loyamba la mwezi wachitatu chichokere mʼdziko la Igupto.


Koma mabanja a fuko la Levi okha sanawawerenge pamodzi ndi ena.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa