Numeri 26:9 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 ndipo ana a Eliabu anali Nemueli, Datani ndi Abiramu. Datani ndi Abiramu anali gulu la akuluakulu aja amene anawukira Mose ndi Aaroni ndipo analinso mʼgulu la otsatira Kora pamene anawukira Yehova. Onani mutuwoBuku Lopatulika9 Ndi ana a Eliyabu: Nemuwele, ndi Datani ndi Abiramu. Iwo ndiwo Datani ndi Abiramu omwe aja oitanidwa a khamu, amene anatsutsana ndi Mose ndi Aroni mu msonkhano wa Kora, muja anatsutsana ndi Yehova; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndi ana a Eliyabu: Nemuwele, ndi Datani ndi Abiramu. Iwo ndiwo Datani ndi Abiramu omwe aja oitanidwa a khamu, amene anatsutsana ndi Mose ndi Aroni mu msonkhano wa Kora, muja anatsutsana ndi Yehova; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 ndipo ana a Eliyabu anali Nemuwele, Datani ndi Abiramu. Ameneŵa anali omwe aja amene adasankhidwa mu mpingo, amenenso adakangana ndi Mose ndi Aroni pogwirizana ndi Kora, pamene adatsutsana ndi Chauta. Onani mutuwo |