Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 2:22 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

22 Lotsatira lidzakhala fuko la Benjamini. Mtsogoleri wa Abenjamini ndi Abidani mwana wa Gideoni.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

22 Ndi fuko la Benjamini: kalonga wa ana a Benjamini ndiye Abidani mwana wa Gideoni.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

22 Ndi fuko la Benjamini: kalonga wa ana a Benjamini ndiye Abidani mwana wa Gideoni.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

22 Tsono pabwere fuko la Benjamini, limene mtsogoleri wake ndi Abidani mwana wa Gideoni,

Onani mutuwo Koperani




Numeri 2:22
7 Mawu Ofanana  

Pali fuko lalingʼono la Benjamini, kuwatsogolera, pali gulu lalikulu la ana a mafumu a Yuda, ndiponso pali ana a mafumu a Zebuloni ndi Nafutali.


Abidani mwana wa Gideoni, kuchokera ku fuko la Benjamini,


Abidani mwana wa Gideoni ndiye anali mtsogoleri wa mtundu wa Benjamini.


Chiwerengero cha gulu lake lankhondo ndi 32,200.


Chiwerengero cha gulu lake lankhondo ndi 35,400.


Pa tsiku lachisanu ndi chinayi Abidani mwana wa Gideoni mtsogoleri wa fuko la Benjamini, anabweretsa chopereka chake.


ngʼombe zazimuna ziwiri, nkhosa zazimuna zisanu, mbuzi zazimuna zisanu, ndi ana ankhosa aamuna asanu a chaka chimodzi, nsembe yachiyanjano. Ichi chinali chopereka cha Abidani mwana wa Gideoni.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa