Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 2:12 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

12 Fuko la Simeoni lidzamanga pafupi ndi Rubeni. Mtsogoleri wa gulu la Simeoni ndi Selumieli mwana wa Zurisadai.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

12 Ndipo iwo akumanga mahema ao poyandikizana naye ndiwo a fuko la Simeoni; ndi kalonga wa ana a Simeoni ndiye Selumiele mwana wa Zurishadai.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

12 Ndipo iwo akumanga mahema ao poyandikizana naye ndiwo a fuko la Simeoni; ndi kalonga wa ana a Simeoni ndiye Selumiele mwana wa Zurishadai.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

12 Amene amange pafupi ndi fuko lake akhale a fuko la Simeoni, limene mtsogoleri wake ndi Selumiele mwana wa Zurishadai,

Onani mutuwo Koperani




Numeri 2:12
6 Mawu Ofanana  

Selumieli mwana wa Zurisadai, kuchokera ku fuko la Simeoni,


Mtsogoleri wa fuko la Simeoni anali Selumieli mwana wa Zurisadai,


Chiwerengero cha gulu lake lankhondo ndi 46,500.


Chiwerengero cha gulu lake lankhondo ndi 59,300.


Pa tsiku lachisanu Selumieli mwana wa Zurisadai, mtsogoleri wa fuko la Simeoni, anabweretsa chopereka chake.


ngʼombe ziwiri, nkhosa zisanu, mbuzi zazimuna zisanu ndi ana ankhosa aamuna asanu a chaka chimodzi, nsembe yachiyanjano. Ichi chinali chopereka cha Selumieli mwana wa Zurisadai.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa