Numeri 19:3 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Muyipereke kwa Eliezara, wansembe ndipo apite nayo kunja kwa msasa. Iphedwe iye ali pomwepo. Onani mutuwoBuku Lopatulika3 ndipo muipereke kwa Eleazara wansembe, naitulutse iye kunja kwa chigono, ndipo wina aiphe pamaso pake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 ndipo muipereke kwa Eleazara wansembe, naitulutse iye kunja kwa chigono, ndipo wina aiphe pamaso pake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Muupereke kwa wansembe Eleazara, kenaka anthu atuluke nawo kunja kwa mahema, ndipo auphe pamaso pake. Onani mutuwo |