Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 13:10 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

10 kuchokera ku fuko la Zebuloni, Gadieli mwana wa Sodi;

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

10 Wa fuko la Zebuloni, Gadiele mwana wa Sodi.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

10 Wa fuko la Zebuloni, Gadiele mwana wa Sodi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

10 M'fuko la Zebuloni, adatuma Gadiele mwana wa Sodi.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 13:10
2 Mawu Ofanana  

kuchokera ku fuko la Manase (fuko la Yosefe), Gadi mwana wa Susi;


kuchokera ku fuko la Benjamini, Paliti mwana wa Rafu;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa