Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 12:4 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

4 Nthawi yomweyo Yehova anati kwa Mose, Aaroni ndi Miriamu, “Bwerani ku tenti ya msonkhano nonse atatu.” Ndipo atatuwo anapitadi kumeneko.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

4 Ndipo Yehova anati kwa Mose, ndi Aroni, ndi Miriyamu modzidzimutsa, Tulukani inu atatu kudza ku chihema chokomanako. Pamenepo anatuluka atatuwo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

4 Ndipo Yehova anati kwa Mose, ndi Aroni, ndi Miriyamu modzidzimutsa, Tulukani inu atatu kudza ku chihema chokomanako. Pamenepo anatuluka atatuwo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

4 Tsono Chauta adauza Mose, Aroni ndi Miriyamu kuti, “Atatu nonsenu mubwere ku chihema chamsonkhano.” Ndipo onse atatuwo adapitadi.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 12:4
5 Mawu Ofanana  

pamene Inu Mulungu munadzuka kuti muweruze, kupulumutsa onse osautsidwa mʼdziko. Sela


Yehova anayankhula ndi Mose mʼchipululu cha Sinai, mu tenti ya msonkhano, pa tsiku loyamba la mwezi wachiwiri, mʼchaka chachiwiri atatuluka mu Igupto, kuti,


(Koma Mose anali munthu wodzichepetsa kwambiri kuposa munthu aliyense pa dziko lapansi).


Tsono Yehova anatsika mu mtambo, nayima pa khomo la chihema. Kenaka anayitana Aaroni ndi Miriamu. Ndipo onse awiri atapita patsogolo,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa