Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 10:18 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

18 Kenaka magulu a msasa wa fuko la Rubeni ananyamuka potsatira mbendera yawo. Mtsogoleri wawo anali Elizuri mwana wa Sedeuri.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

18 Ndi a mbendera ya chigono cha Rubeni, anayenda monga mwa magulu ao; ndipo pa gulu lake anayang'anira Elizuri mwana wa Sedeuri.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

18 Ndi a mbendera ya chigono cha Rubeni, anayenda monga mwa magulu ao; ndipo pa gulu lake anayang'anira Elizuri mwana wa Sedeuri.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

18 Pambuyo pake otsata mbendera ya zithando za fuko la Rubeni adanyamuka m'magulumagulu, ndipo mtsogoleri wa gulu lao anali Elizuri mwana wa Sedeuri.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 10:18
6 Mawu Ofanana  

Mayina a anthu amene akuthandizeniwo ndi awa: Elizuri mwana wa Sedeuri, kuchokera ku fuko la Rubeni,


Mtsogoleri wa fuko la Simeoni anali Selumieli mwana wa Zurisadai,


Akaliza lipenga lochenjeza lachiwiri, misasa yakummwera iyambe kusamuka. Kuliza kwa lipenga lochenjeza kudzakhala chizindikiro choyamba ulendo.


ndi ngʼombe zazimuna ziwiri, nkhosa zazimuna ziwiri, mbuzi zazimuna zisanu ndi ana ankhosa aamuna asanu a chaka chimodzi, nsembe yachiyanjano. Ichi chinali chopereka cha Elizuri mwana wa Sedeuri.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa