Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 1:42 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

42 Kuchokera mwa zidzukulu za Nafutali: Aamuna onse a zaka makumi awiri kapena kupitirirapo, omwe akanatha kugwira ntchito ya usilikali anawalemba mayina awo monga mwa mbiri ya mafuko awo ndi mabanja awo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

42 A ana a Nafutali, kubadwa kwao, monga mwa mabanja ao, monga mwa nyumba za makolo ao, powerenga maina, kuyambira a zaka makumi awiri ndi mphambu, onse akutulukira kunkhondo;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

42 A ana a Nafutali, kubadwa kwao, monga mwa mabanja ao, monga mwa nyumba za makolo ao, powerenga maina, kuyambira a zaka makumi awiri ndi mphambu, onse akutulukira kunkhondo;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

42 Mwa zidzukulu za Nafutali adalemba maina a amuna onse otha kumenya nkhondo, a zaka 20 ndi a zaka zopitirirapo, potsata mabanja ao ndiponso banja la makolo ao.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 1:42
6 Mawu Ofanana  

Ana aamuna a Nafutali ndi awa: Yahazeeli, Guni, Yezeri ndi Silemu.


“Nafutali ali ngati mbawala yayikazi yokhala ndi ana okongola kwambiri.


Chiwerengero cha anthu ochokera mʼfuko la Aseri chinali 41,500.


Chiwerengero cha anthu ochokera mʼfuko la Nafutali chinali 53,400.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa