Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 1:41 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

41 Chiwerengero cha anthu ochokera mʼfuko la Aseri chinali 41,500.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

41 owerengedwa ao a fuko la Asere, ndiwo zikwi makumi anai mphambu chimodzi kudza mazana asanu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

41 owerengedwa ao a fuko la Asere, ndiwo zikwi makumi anai mphambu chimodzi kudza mazana asanu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

41 Tsono ataŵerenga maina onse a m'fuko la Asere, adapezeka kuti ali 41,500.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 1:41
4 Mawu Ofanana  

Kuchokera mwa zidzukulu za Aseri: Amuna onse a zaka makumi awiri kapena kupitirirapo, omwe akanatha kugwira ntchito ya usilikali anawalemba mayina awo monga mwa mbiri ya mafuko awo ndi mabanja awo.


Kuchokera mwa zidzukulu za Nafutali: Aamuna onse a zaka makumi awiri kapena kupitirirapo, omwe akanatha kugwira ntchito ya usilikali anawalemba mayina awo monga mwa mbiri ya mafuko awo ndi mabanja awo.


Chiwerengero cha gulu lake lankhondo ndi 41,500.


Awa ndiwo anali mafuko a Aseri. Onse amene anawerengedwa analipo 53,400.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa