Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 1:40 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

40 Kuchokera mwa zidzukulu za Aseri: Amuna onse a zaka makumi awiri kapena kupitirirapo, omwe akanatha kugwira ntchito ya usilikali anawalemba mayina awo monga mwa mbiri ya mafuko awo ndi mabanja awo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

40 A ana a Asere, kubadwa kwao, monga mwa mabanja ao, monga mwa nyumba za makolo ao, powerenga maina, kuyambira a zaka makumi awiri ndi mphambu, onse akutulukira kunkhondo;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

40 A ana a Asere, kubadwa kwao, monga mwa mabanja ao, monga mwa nyumba za makolo ao, powerenga maina, kuyambira a zaka makumi awiri ndi mphambu, onse akutulukira kunkhondo;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

40 Mwa zidzukulu za Asere adalemba maina a amuna onse otha kumenya nkhondo, a zaka 20 ndi a zaka zopitirirapo, potsata mabanja ao ndiponso banja la makolo ao.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 1:40
6 Mawu Ofanana  

Pophatikiza ana awiri a Yosefe obadwira ku Igupto, anthu a pa banja la Yakobo amene anapita ku Igupto, onse pamodzi analipo 70.


“Dziko la Aseri lidzabereka chakudya chokoma, ndipo iye adzapereka chakudya kwa mafumu.


Chiwerengero cha anthu ochokera mʼfuko la Dani chinali 62,700.


Chiwerengero cha anthu ochokera mʼfuko la Aseri chinali 41,500.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa