Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 1:39 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

39 Chiwerengero cha anthu ochokera mʼfuko la Dani chinali 62,700.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

39 owerengedwa ao a fuko la Dani, ndiwo zikwi makumi asanu ndi limodzi mphambu ziwiri kudza mazana asanu ndi awiri.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

39 owerengedwa ao a fuko la Dani, ndiwo zikwi makumi asanu ndi limodzi mphambu ziwiri kudza mazana asanu ndi awiri.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

39 Tsono ataŵerenga maina onse a m'fuko la Dani, adapezeka kuti ali 62,700.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 1:39
4 Mawu Ofanana  

Kuchokera mwa zidzukulu za Dani: Amuna onse a zaka makumi awiri kapena kupitirirapo, omwe akanatha kugwira ntchito ya usilikali anawalemba mayina awo monga mwa mbiri ya mafuko awo ndi mabanja awo.


Kuchokera mwa zidzukulu za Aseri: Amuna onse a zaka makumi awiri kapena kupitirirapo, omwe akanatha kugwira ntchito ya usilikali anawalemba mayina awo monga mwa mbiri ya mafuko awo ndi mabanja awo.


Chiwerengero cha gulu lake lankhondo ndi 62,700.


Onse a fuko la Asuhamu amene anawerengedwa analipo 64,400.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa