Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 1:23 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

23 Chiwerengero cha anthu ochokera mʼfuko la Simeoni chinali 59,300.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

23 owerengedwa ao a fuko la Simeoni, ndiwo zikwi makumi asanu mphambu zisanu ndi zinai kudza mazana atatu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

23 owerengedwa ao a fuko la Simeoni, ndiwo zikwi makumi asanu mphambu zisanu ndi zinai kudza mazana atatu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

23 Tsono ataŵerenga maina onse a m'fuko la Simeoni, adapezeka kuti ali 59,300.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 1:23
6 Mawu Ofanana  

Kuchokera mwa zidzukulu za Simeoni: Amuna onse a zaka makumi awiri kapena kupitirirapo, omwe akanatha kugwira ntchito ya usilikali anawalemba mayina awo, mmodzimmodzi monga mwa mbiri ya mafuko awo ndi mabanja awo.


Kuchokera mwa zidzukulu za Gadi: Amuna onse a zaka makumi awiri kapena kupitirirapo, omwe akanatha kugwira ntchito ya usilikali anawalemba mayina awo monga mwa mbiri ya mafuko awo ndi mabanja awo.


Chiwerengero cha gulu lake lankhondo ndi 59,300.


Dzina la Mwisraeli yemwe anaphedwa ndi mkazi wa Chimidiyani anali Zimuri mwana wa Salu, mtsogoleri wa banja la Simeoni.


Awa anali mafuko a Simeoni. Iwowa analipo amuna 22,200.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa