Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 1:15 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

15 Ahira mwana wa Enani, kuchokera ku fuko la Nafutali.”

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

15 Wa Nafutali, Ahira mwana wa Enani.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

15 Wa Nafutali, Ahira mwana wa Enani.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

15 fuko la Nafutali, Ahira mwana wa Enani.”

Onani mutuwo Koperani




Numeri 1:15
5 Mawu Ofanana  

Eliyasafu mwana wa Deuweli, kuchokera ku fuko la Gadi,


Amenewa ndi anthu amene anasankhidwa kuchokera mʼmagulu mwawo, eni mbumba a mafuko a makolo awo. Iwowa anali atsogoleri a mafuko a Israeli.


ndipo mtsogoleri wa mtundu wa Nafutali anali Ahira mwana wa Enani.


Lotsatira lidzakhala fuko la Nafutali. Mtsogoleri wa Anafutali ndi Ahira mwana wa Enani.


Pa tsiku la khumi ndi chimodzi Ahira mwana wa Enani, mtsogoleri wa fuko la Nafutali, anabweretsa chopereka chake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa