Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Genesis 7:6 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

6 Pamene chigumula chinabwera pa dziko lapansi Nowa anali ndi zaka 600.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

6 Ndipo Nowa anali wa zaka mazana asanu ndi limodzi, pamene chigumula cha madzi chinali padziko lapansi.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

6 Ndipo Nowa anali wa zaka mazana asanu ndi limodzi, pamene chigumula cha madzi chinali pa dziko lapansi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

6 Nowa anali wa zaka 600 pamene chigumulacho chidafika pa dziko lapansi.

Onani mutuwo Koperani




Genesis 7:6
4 Mawu Ofanana  

Pamene Nowa anali ndi zaka 500, anabereka Semu, Hamu ndi Yafeti.


Pa tsiku la 17 la mwezi wachiwiri, Nowa ali ndi zaka 600, akasupe onse akuya kwambiri anasefuka ndiponso zitseko za madzi akumwamba zinatsekuka.


Pofika tsiku loyamba la mwezi woyamba wa chaka chimene Nowa anakwanitsa zaka 601, madzi anawuma pa dziko lapansi. Ndipo Nowa anachotsa denga la chombo ndipo anaona kuti kunja kwawuma.


Monga momwe zinalili nthawi ya Nowa, momwemonso zidzatero pobwera kwa Mwana wa Munthu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa