Genesis 3:2 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Mkaziyo anati kwa njokayo, “Tikhoza kudya zipatso za mʼmitengo ya mʼmundawu, Onani mutuwoBuku Lopatulika2 Mkaziyo ndipo anati kwa njoka, Zipatso za mitengo ya m'mundamu tidye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Mkaziyo ndipo anati kwa njoka, Zipatso za mitengo ya m'mundamu tidye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Mkazi uja adayankha kuti, “Tingathe kudya zipatso za mtengo uliwonse m'munda muno, Onani mutuwo |