Eksodo 8:18 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Koma amatsenga atayesa kupanga nsabwe mwa matsenga awo, analephera. Ndipo nsabwezo zinali pa munthu aliyense ndi pa ziweto zawo. Onani mutuwoBuku Lopatulika18 Alembi anateronso ndi matsenga ao kuonetsa nsabwe, koma sanakhoze; ndipo panali nsabwe pa anthu, ndi pa zoweta. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Alembi anateronso ndi matsenga ao kuonetsa nsabwe, koma sanakhoza; ndipo panali nsabwe pa anthu, ndi pa zoweta. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Amatsenga aja adayesanso momwemo mwa matsenga ao kuti apange zao nthata, koma adalephera. Ndipo nthatazo zidabalalikira pa anthu ndi nyama zomwe. Onani mutuwo |