Eksodo 5:9 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Muwakhawulitse ndi ntchito anthu amenewa kuti azitanganidwa, asakhale ndi mpata omvera zabodza.” Onani mutuwoBuku Lopatulika9 Ilimbike ntchito pa amunawo, kuti aigwiritsitse, asasamalire mau amabodza. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ilimbike ntchito pa amunawo, kuti aigwiritsitse, asasamalire mau amabodza. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Muŵagwiritse ntchito yakalavulagaga anthu ameneŵa, kuti azitanganidwa ndi ntchito m'malo momangomvera zabodza.” Onani mutuwo |