Eksodo 5:7 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 “Inu musawapatsenso udzu wopangira njerwa monga mumachitira kale, iwo azipita ndi kukatenga udzu wawo. Onani mutuwoBuku Lopatulika7 Musawapatsanso anthu udzu wakupanga nao njerwa monga kale; apite okha adzifunire udzu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Musawapatsanso anthu udzu wakupanga nao njerwa monga kale; apite okha adzifunire udzu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 “Musaŵapatsenso udzu wa njerwa anthu ameneŵa, monga muja munkachitiramu. Alekeni azikamweta okha udzuwo. Onani mutuwo |