Eksodo 4:19 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Nthawiyi Yehova anali atamuwuza kale Mose ku Midiyani kuti, “Bwerera ku Igupto, pakuti anthu onse amene amafuna kukupha aja anamwalira.” Onani mutuwoBuku Lopatulika19 Ndipo Yehova ananena ndi Mose mu Midiyani, Muka, bwerera kunka ku Ejipito; pakuti adafa anthu onse amene anafuna moyo wako. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Ndipo Yehova ananena ndi Mose m'Midiyani, Muka, bwerera kunka ku Ejipito; pakuti adafa anthu onse amene anafuna moyo wako. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Chauta adauza Mose ku Midiyani kuja kuti, “Bwerera ku Ejipito tsopano popeza kuti onse aja ankafuna kukuphaŵa adamwalira.” Onani mutuwo |