Eksodo 39:4 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Iwo anapanga efodi imene inali ndi timalamba tiwiri ta pa mapewa, tosokerera ku msonga zake ziwiri kuti azitha kumanga. Onani mutuwoBuku Lopatulika4 Anapangira efodi zapamapewa zolumikizana; pansonga ziwirizo anamlumikiza. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Anapangira efodi zapamapewa zolumikizana; pa nsonga ziwirizo anamlumikiza. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Tsono adapanga tizikwewo tam'mapewa ta chovala cha efodi chija, tolumikizika ku chovalacho pa mbali zake ziŵiri. Onani mutuwo |