Eksodo 38:2 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Anapanga nyanga imodziimodzi pa ngodya zake zinayizo, kotero kuti nyangazo ndi guwalo zinali chinthu chimodzi, ndipo anakuta guwalo ndi mkuwa. Onani mutuwoBuku Lopatulika2 Ndipo anapanga nyanga zake pangodya zake zinai; nyanga zake zinakhala zotuluka m'mwemo; ndipo analikuta ndi mkuwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndipo anapanga nyanga zake pangodya zake zinai; nyanga zake zinakhala zotuluka m'mwemo; ndipo analikuta ndi mkuwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Pa ngodya zake zinai adapangapo nyanga zotuluka m'guwalo, mwakuti zidangolumikizika nkukhala chinthu chimodzi ndi guwalo. Ndipo guwa lonselo adalikuta ndi mkuŵa. Onani mutuwo |