Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Eksodo 30:5 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 Upange mizati yamtengo wa mkesha ndipo uyikute ndi golide.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

5 Ndipo upange mphiko za mtengo wakasiya, ndi kuzikuta ndi golide.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Ndipo upange mphiko za mtengo wakasiya, ndi kuzikuta ndi golide.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Mphiko zimenezi ikhale ya mtengo wa kasiya, ndipo uikute ndi golide.

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 30:5
5 Mawu Ofanana  

Kenaka upange mizati yamtengo wa mkesha ndi kuzikuta ndi golide.


Mphetezo uziyike kufupi ndi feremu kuti azikolowekamo nsichi zonyamulira tebuloyo.


zikopa za nkhosa zazimuna za utoto wofiira ndi zikopa za akatumbu; matabwa amtengo wa mkesha;


Upange mphete ziwiri zagolide ndipo uzilumikize ku guwa mʼmunsi mwa mkombero, mphete ziwiri ku mbali zonse ziwiri zoyangʼanana. Mphetozo zizigwira nsichi zonyamulira guwalo.


Uyike guwalo patsogolo pa nsalu yotchinga Bokosi la Chipangano. Apa ndi pamene ndizidzakumana nawe.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa