Eksodo 3:5 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Mulungu anati, “Usayandikire kuno. Vula nsapato zako, pakuti malo amene wayimapo ndi opatulika.” Onani mutuwoBuku Lopatulika5 Ndipo Iye anati, Usayandikire kuno; vula nsapato zako ku mapazi ako, pakuti pamalo pamene upondapo iwe, mpopatulika. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Ndipo Iye anati, Usayandikire kuno; vula nsapato zako ku mapazi ako, pakuti pamalo pamene upondapo iwe, mpopatulika. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Mulungu adati, “Usayandikire pafupi. Vula nsapato zakozo, chifukwa malo waimapowo ngoyera.” Onani mutuwo |