Eksodo 27:12 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 “Mbali yakumadzulo ya bwalolo ikhale yotalika mamita 23 ndipo ikhale ndi nsalu yotchinga, nsichi khumi ndi matsinde khumi. Onani mutuwoBuku Lopatulika12 Ndipo m'kupingasa kwa bwaloli pa mbali ya kumadzulo mukhale nsalu zotchingira za mikono makumi asanu; nsichi zake zikhale khumi, ndi makamwa ao khumi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndipo m'kupingasa kwa bwaloli pa mbali ya kumadzulo mukhale nsalu zochingira za mikono makumi asanu; nsichi zake zikhale khumi, ndi makamwa ao khumi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Muufupi mwake mwa bwalolo cha mbali yakuzambwe, pakhale nsalu zochinga, kutalika kwake mamita 23, ndi nsanamira khumi ndi masinde khumi. Onani mutuwo |