Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Eksodo 26:12 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

12 Theka lotsalira la nsaluyo lidzalendewera kumbuyo kwa chihemacho.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

12 Ndipo chotsalacho pansalu yophimbayo, hafu yake ya nsalu yotsalirayo, itchinge pambuyo pake pa chihemacho.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

12 Ndipo chotsalacho pa nsalu za hemalo, hafu yake ya nsalu yotsalirayo, ichinge pambuyo pake pa Kachisi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

12 Theka la nsalu yotsalira ija idzalendeŵera kumbuyo kwa chihemacho.

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 26:12
3 Mawu Ofanana  

Kenaka upange ngowe 50 zamkuwa ndipo uzilowetse mu zokolowekazo. Ndiye uphatikize nsalu ziwirizo kuti tentiyo ikhale imodzi.


Nsalu yotsalira ya masentimita 46 mulitali mwake mʼmbali zonse ziwiri idzalendewere kuphimba mbali ziwirizo.


“Upange nsalu za ubweya wambuzi zophimba pamwamba pa chihemacho. Nsalu zonse pamodzi zikhale khumi ndi imodzi.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa