Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Eksodo 21:12 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

12 “Munthu aliyense amene amenya mnzake namupha, iyenso ayenera kuphedwa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

12 Iye amene akantha munthu kotero kuti wafa, aphedwe ndithu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

12 Iye amene akantha munthu kotero kuti wafa, aphedwe ndithu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

12 “Munthu aliyense amene amenya mnzake namupha, nayenso aphedwe ndithu.

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 21:12
11 Mawu Ofanana  

Aliyense wopha munthu adzaphedwa, nyama iliyonse yopha munthu idzaphedwa, munthu aliyense wopha munthu mnzake, adzaphedwa.


“Aliyense wopha munthu, adzaphedwanso ndi munthu; pakuti Mulungu analenga munthu mʼchifanizo chake.


Kenaka Davide anati kwa Natani, “Ine ndachimwira Yehova.” Natani anayankha kuti, “Yehova wachotsa tchimo lanu. Simufa ayi.


Koma ngati sangathe kumuchitira zonsezi, ndiye amuleke apite popanda kulipira kanthu.


“ ‘Ngati munthu wina aliyense achotsa moyo wa munthu mnzake, munthuyo ayenera kuphedwa.


Yesu anati kwa iye, “Bwezera lupanga lako mʼchimake, chifukwa onse amene amapha ndi lupanga adzafa ndi lupanga.


“Ndi wotembereredwa munthu amene apha mnzake mwachinsinsi.” Pamenepo anthu onse adzati, “Ameni!”


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa