Eksodo 2:12 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Atayangʼana uku ndi uku, naona kuti panalibe wina aliyense, Mose anamupha Mwiguptoyo ndipo anamukwirira mu mchenga. Onani mutuwoBuku Lopatulika12 Ndipo anaunguza kwina ndi kwina, ndipo pamene anaona kuti palibe munthu, anakantha Mwejipito, namfotsera mumchenga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndipo anaunguza kwina ndi kwina, ndipo pamene anaona kuti palibe munthu, anakantha Mwejipito, namfotsera mumchenga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Pamenepo Mose atayang'ana uku ndi uku, naona kuti kulibe anthu, adamupha Mwejipitoyo, nafotsera mtembo wake mu mchenga. Onani mutuwo |